Masalimo 109:16 - Buku Lopatulika16 Chifukwa kuti sanakumbukire kuchita chifundo, koma analondola wozunzika ndi waumphawi, ndi wosweka mtima, kuti awaphe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Chifukwa kuti sanakumbukire kuchita chifundo, koma analondola wozunzika ndi waumphawi, ndi wosweka mtima, kuti awaphe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Pakuti munthuyo sadakumbukire kuchita chifundo, koma adazunza osauka, osoŵa ndi ovutika mu mtima, mpaka kuŵapha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Pakuti iye sanaganizirepo zochita chifundo, koma anazunza mpaka kuwapha anthu osauka ndi osweka mtima. Onani mutuwo |