Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 109:15 - Buku Lopatulika

15 Zikhale pamaso pa Yehova chikhalire, kuti adule chikumbukiro chao kuchichotsera kudziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Zikhale pamaso pa Yehova chikhalire, kuti adule chikumbukiro chao kuchichotsera kudziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Chauta asakhululukire machimowo mpaka muyaya, anthuwo aiŵalike pa dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Machimo awo akhale pamaso pa Yehova nthawi zonse, kuti Iye achotse chikumbutso chawo pa dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 109:15
11 Mawu Ofanana  

Chikumbukiro chake chidzatayika m'dziko, ndipo adzasowa dzina kukhwalala.


Zidzukulu zake zidulidwe; dzina lao lifafanizidwe mu mbadwo ukudza.


Nkhope ya Yehova itsutsana nao akuchita zoipa, kudula chikumbukiro chao padziko lapansi.


Iwowo anaitana, ndipo Yehova anawamva, nawalanditsa kumasautso ao onse.


Muzibisire nkhope yanu zolakwa zanga, ndipo mufafanize mphulupulu zanga zonse.


Munaika mphulupulu zathu pamaso panu, ndi zoipa zathu zobisika pounikira nkhope yanu.


Ndipo mudzasiya dzina lanu likhale chitemberero kwa osankhidwa anga, ndipo Ambuye Yehova adzakupha iwe, nadzatcha atumiki ake dzina lina;


Pakuti ngakhale usamba ndi soda, ndi kudzitengera sopo wambiri, mphulupulu zako zidziwika pamaso panga, ati Yehova Mulungu.


Ndipo sanena m'mtima mwao kuti Ine ndikumbukira zoipa zao zonse; tsopano machitidwe ao awazinga; ali pamaso panga.


Yehova walumbira pali kudzikuza kwa Yakobo, Ngati ndidzaiwala konse ntchito zao zilizonse?


Kodi sichisungika ndi Ine, cholembedwa chizindikiro mwa chuma changa chenicheni?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa