Masalimo 109:13 - Buku Lopatulika13 Zidzukulu zake zidulidwe; dzina lao lifafanizidwe mu mbadwo ukudza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Zidzukulu zake zidulidwe; dzina lao lifafanizidwe mu mbadwo ukudza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Zidzukulu zake zithe nkufa, dzina lao lisamvekenso mu mbadwo wachiŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Zidzukulu zake zithe nʼkufa, mayina awo afafanizidwe mu mʼbado wotsatirawo. Onani mutuwo |