Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 103:14 - Buku Lopatulika

14 Popeza adziwa mapangidwe athu; akumbukira kuti ife ndife fumbi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Popeza adziwa mapangidwe athu; akumbukira kuti ife ndife fumbi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Amadziŵa m'mene adatipangira, amakumbukira kuti ife ndife fumbi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 pakuti Iye amadziwa momwe tinawumbidwira, amakumbukira kuti ndife fumbi.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 103:14
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Yehova Mulungu anaumba munthu ndi dothi lapansi, nauzira mpweya wa moyo m'mphuno mwake; munthuyo nakhala wamoyo.


m'thukuta la nkhope yako udzadya chakudya, kufikira kuti udzabwerera kunthaka: chifukwa kuti m'menemo unatengedwa: chifukwa kuti ndiwe fumbi, ndi kufumbiko udzabwerera.


Mukumbukire kuti mwandiumba ngati dothi; ndipo kodi mudzandibwezera kufumbi?


Kodi mudzaopsa tsamba lakungouluka, ndi kulondola ziputu zouma?


Mulekeranji kukhululukira kulakwa kwanga ndi kundichotsera mphulupulu yanga? Popeza tsopano ndidzagona kufumbi; mudzandifunafuna, koma ine palibe.


Kumbukirani kuti nthawi yanga njapafupi; munalengeranji ana onse a anthu kwachabe?


fumbi ndi kubwera pansi pomwe linali kale, mzimu ndi kubwera kwa Mulungu amene anaupereka.


Ozolitsa inu! Kodi woumba adzayesedwa ngati dothi; kodi chinthu chopangidwa chinganene za iye amene anachipanga, Iye sanandipange ine konse; kapena kodi chinthu choumbidwa chinganene za iye amene anachiumba, Iye alibe nzeru?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa