Masalimo 100:4 - Buku Lopatulika4 Lowani kuzipata zake ndi chiyamiko, ndi kumabwalo ake ndi chilemekezo: Myamikeni; lilemekezeni dzina lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Lowani kuzipata zake ndi chiyamiko, ndi kumabwalo ake ndi chilemekezo: Myamikeni; lilemekezeni dzina lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Loŵani pa zipata zake mukuthokoza, pitani m'mabwalo a Nyumba yake mukutamanda. Yamikani Chauta, lemekezani dzina lake! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Lowani ku zipata zake ndi chiyamiko ndi ku mabwalo ake ndi matamando; muyamikeni ndi kutamanda dzina lake. Onani mutuwo |