Masalimo 10:15 - Buku Lopatulika15 Thyolani mkono wa woipa; ndipo wochimwa, mutsate choipa chake kufikira simuchipezanso china. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Thyolani mkono wa woipa; ndipo wochimwa, mutsate choipa chake kufikira simuchipezanso china. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Thetsani mphamvu za munthu woipa ndi wochimwa. Fufuzani kuipa kwake, ndipo mumlange kuti asadzabwerezenso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Thyolani dzanja la woyipitsitsa ndi la munthu woyipa; muzengeni mlandu chifukwa cha zoyipa zake zimene sizikanadziwika. Onani mutuwo |