Marko 9:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anawafunsa iwo, Mufunsana nao chiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anawafunsa iwo, Mufunsana nao chiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Iye adaŵafunsa kuti, “Kodi mukutsutsana zotani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Iye anafunsa kuti, “Mukukangana nawo chiyani iwowa?” Onani mutuwo |