Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 9:13 - Buku Lopatulika

13 Koma ndinena ndi inu kuti anafikadi Eliya, ndipo anamchitiranso zilizonse iwo anazifuna, monga kwalembedwa za iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Koma ndinena ndi inu kuti anafikadi Eliya, ndipo anamchitiranso zilizonse iwo anazifuna, monga kwalembedwa za iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Ine ndikukuuzani kuti Eliya adafikadi, ndipo anthu adamchita zonse zomwe iwo ankafuna, monga momwe Malembo adaanenera za iye.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Koma ndikuwuzani, kuti Eliya wabweradi, ndipo amuchitira iye zonse zimene iwo anafuna, monga momwe zalembedwera za iye.”

Onani mutuwo Koperani




Marko 9:13
9 Mawu Ofanana  

Ndipo ngati mufuna kulandira, uyu ndiye Eliya amene amati akudza.


Ndipo Iye ananena nao, Eliya ayamba kudza ndithu, nadzakonza zinthu zonse; ndipo kwalembedwa bwanji za Mwana wa Munthu, kuti ayenera kumva zowawa zambiri ndi kuyesedwa chabe?


Ndipo pamene anadza kwa ophunzira, anaona khamu lalikulu la anthu ozungulira iwo, ndi alembi alikufunsana nao.


Ndipo adzamtsogolera Iye, ndi mzimu ndi mphamvu ya Eliya, kutembenuzira mitima ya atate kwa ana ao, ndi osamvera kuti atsate nzeru ya olungama mtima; kukonzeratu Ambuye anthu okonzeka.


Ndiye yani wa aneneri makolo anu sanamzunze? Ndipo anawapha iwo amene anaonetseratu za kudza kwake kwa Wolungamayo; wa Iye amene mwakhala tsopano akumpereka ndi akumupha;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa