Marko 8:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo anali nato tinsomba towerengeka; ndipo Iye anatidalitsa, nati atipereke itonso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo anali nato tinsomba towerengeka; ndipo Iye anatidalitsa, nati atipereke itonso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Adaalinso ndi tinsomba toŵerengeka. Yesu adathokoza Mulungu chifukwa cha tinsombato, nalamula ophunzira ake kuti atiperekenso kwa anthu aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Analinso ndi tinsomba tochepa; Iye anayamikanso chifukwa cha nsombazo. Ndipo anawuza ophunzira kuti awagawire. Onani mutuwo |