Marko 8:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo ophunzira adaiwala kutenga mikate, ndipo analibe mkate m'ngalawa koma umodzi wokha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo ophunzira adaiwala kutenga mikate, ndipo analibe mkate m'ngalawa koma umodzi wokha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Ophunzira a Yesu anali ataiŵala kutenga buledi, kotero kuti m'chombomo adaali ndi buledi mmodzi yekha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ophunzira anayiwala kutenga buledi, kupatula buledi mmodzi yekha amene anali naye mʼbwato. Onani mutuwo |