Marko 7:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo anadza naye kwa Iye munthu wogontha, ndi wachibwibwi; ndipo anampempha Iye kuti aike dzanja pa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo anadza naye kwa Iye munthu wogontha, ndi wachibwibwi; ndipo anampempha Iye kuti aike dzanja pa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Anthu ena adabwera kwa Iye ndi munthu yemwe anali gonthi ndi wolankhula movutikira. Anthuwo adapempha Yesu kuti amchiritse pomusanjika manja munthuyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Kumeneko anthu ena anabweretsa kwa Iye munthu amene anali wosamva ndi wosayankhula, ndipo anamupempha kuti asanjike dzanja pa iye. Onani mutuwo |