Marko 7:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo m'mene Iye adalowa m'nyumba kusiyana ndi khamulo, ophunzira ake anamfunsa Iye fanizolo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo m'mene Iye adalowa m'nyumba kusiyana ndi khamulo, ophunzira ake anamfunsa Iye fanizolo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Pamene Yesu adasiya khamu lija la anthu nakaloŵa m'nyumba, ophunzira ake adamufunsa za fanizo limeneli. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Atalisiya gulu la anthu ndi kulowa mʼnyumba, ophunzira ake anamufunsa za fanizoli Onani mutuwo |