Marko 7:12 - Buku Lopatulika12 simulolanso kumchitira kanthu atate wake kapena amai wake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 simulolanso kumchitira kanthu atate wake kapena amai wake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 ameneyo sasoŵanso kuŵathandiza atate ake ndi amai ake.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 pamenepo inu simumalola kuti achitire kanthu kalikonse abambo kapena amayi ake. Onani mutuwo |