Marko 6:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo kumeneko sanakhoze Iye kuchita zamphamvu konse, koma kuti anaika manja ake pa anthu odwala owerengeka, nawachiritsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo kumeneko sanakhoze Iye kuchita zamphamvu konse, koma kuti anaika manja ake pa anthu odwala owerengeka, nawachiritsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Motero sadathe kuchita zinthu zamphamvu kumeneko. Adangosanjika manja pa odwala oŵerengeka, nkuŵachiritsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Sanachite zodabwitsa kumeneko, koma anangosanjika manja pa odwala ochepa ndi kuwachiritsa. Onani mutuwo |