Marko 6:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo ananena nao, Kumene kulikonse mukalowa m'nyumba, khalani komweko kufikira mukachokako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo ananena nao, Kumene kulikonse mukalowa m'nyumba, khalani komweko kufikira mukachokako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Adaŵauzanso kuti, “Mukafika pa mudzi, muzikhala nao kunyumba kumene mudafikirako, mpaka itakwana nthaŵi yoti muchoke kumudziko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pamene mulowa mʼnyumba mukakhale momwemo kufikira mutachoka mʼmudzimo. Onani mutuwo |