Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 5:32 - Buku Lopatulika

32 Ndipo Iye anaunguzaunguza kumuona iye amene adachita ichi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Ndipo Iye anaunguzaunguza kumuona iye amene adachita ichi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Koma Yesu adayang'anayang'ana kuti aone yemwe wachita zimenezo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Koma Yesu anapitirizabe kuyangʼana kuti aone amene anachita zimenezi.

Onani mutuwo Koperani




Marko 5:32
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Yesu anaunguzaunguza, nanena ndi ophunzira ake, Okhala nacho chuma adzalowa mu Ufumu wa Mulungu ndi kuvuta nanga!


Ndipo ophunzira ake ananena kwa Iye, Muona kuti khamu lilikukanikiza Inu, ndipo munena kodi, Wandikhudza ndani?


Koma mkaziyo anachita mantha, ndi kunthunthumira, podziwa chimene anamchitira iye, nadza, namgwadira, namuuza choona chonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa