Marko 5:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo m'mene Iye analikulowa mungalawa, anampempha waziwanda uja kuti akhale ndi Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo m'mene Iye analikulowa mungalawa, anampempha waziwanda uja kuti akhale ndi Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pamene Yesu ankakaloŵa m'chombo, munthu amene adaagwidwa ndi mizimu yoipa uja adampempha kuti apite nao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Yesu akulowa mʼbwato, munthu amene anagwidwa ndi ziwanda uja anamupempha kuti apite nawo. Onani mutuwo |