Marko 5:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo akuziweta anathawa, nauza m'mzinda, ndi kuminda. Ndipo anadza kudzaona chochitikacho. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo akuziweta anathawa, nauza m'mudzi, ndi kuminda. Ndipo anadza kudzaona chochitikacho. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Oŵeta nkhumbazo adathaŵa, nakasimbira anthu mu mzinda ndi ku midzi. Pamenepo anthu adatuluka kuti akaone zimene zidaachitikazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Omwe amaweta nkhumbazo anathawa ndi kukawuza anthu za izi mu mzinda ndi ku madera a ku midzi, ndipo anthu anapita kukaona zomwe zinachitika. Onani mutuwo |