Marko 4:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo ananena, Amene ali nao makutu akumva amve. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo ananena, Amene ali nao makutu akumva amve. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsono Yesu adati, “Yemwe ali ndi makutu akumva, amve!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pamenepo Yesu anati, “Amene ali ndi makutu akumva, amve.” Onani mutuwo |