Marko 4:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo zina zinagwa paminga, ndipo minga inakula, nkuzitsamwitsa, ndipo sizinabale zipatso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo zina zinagwa paminga, ndipo minga inakula, nizitsamwitsa, ndipo sizinabala zipatso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mbeu zina zidagwera pa zitsamba zaminga. Zitsambazo pokula zidalanda chakudya cha mbeu zija, kotero kuti mbeuzo sizidabereke konse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mbewu zina zinagwa pa minga, ndipo mingayo inayanga ndi kuzirepheretsa kukula. Onani mutuwo |