Marko 4:6 - Buku Lopatulika6 ndipo litakwera dzuwa zinapserera; ndipo popeza zinalibe mizu zinakhwinyata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 ndipo litakwera dzuwa zinapserera; ndipo popeza zinalibe mizu zinakhwinyata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Koma pamene dzuŵa lidakwera, zidapserera kenaka zidauma, chifukwa zinali zosazika mizu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Koma dzuwa litakwera, mbewuzo zinapserera, ndipo zinawuma chifukwa zinalibe mizu. Onani mutuwo |