Marko 4:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo ananena nao, Muchitiranji mantha? Kufikira tsopano mulibe chikhulupiriro kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo ananena nao, Muchitiranji mantha? Kufikira tsopano mulibe chikhulupiriro kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Apo Yesu adaŵafunsa kuti, “Bwanji mukuchita mantha? Kani mulibe chikhulupiriro inu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Iye anati kwa ophunzira ake, “Muli ndi mantha chifukwa chiyani? Kodi mukanalibe chikhulupiriro?” Onani mutuwo |