Marko 3:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo anati kwa ophunzira ake, kuti kangalawa kamlinde Iye, chifukwa cha khamulo, kuti angamkanikize Iye, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo anati kwa ophunzira ake, kuti kangalawa kamlinde Iye, chifukwa cha khamulo, kuti angamkanikize Iye, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Yesu adauza ophunzira ake kuti amuikire chombo pafupi, kuwopa kuti anthu angayambe kumpanikiza, chifukwa chidaali chikhamu chachikulu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Chifukwa cha gulu la anthu, anawuza ophunzira ake kuti apezeretu bwato likhale, kuti anthu angamupanikize. Onani mutuwo |