Marko 3:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Yesu anachokako pamodzi ndi ophunzira ake nanka kunyanja: ndipo linamtsata khamu lalikulu la a ku Galileya, ndi a ku Yudeya, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Yesu anachokako pamodzi ndi ophunzira ake nanka kunyanja: ndipo linamtsata khamu lalikulu la a ku Galileya, ndi a ku Yudeya, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Yesu pamodzi ndi ophunzira ake adachokapo napita ku Nyanja ya Galileya. Khamu lalikulu la anthu lidamtsatira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Yesu anachoka pamodzi ndi ophunzira ake napita ku nyanja, ndipo gulu lalikulu la anthu lochokera ku Galileya linamutsata. Onani mutuwo |