Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 3:6 - Buku Lopatulika

6 Ndipo Afarisi anatuluka, ndipo pomwepo anamkhalira upo ndi Aherode, wakumuononga Iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo Afarisi anatuluka, ndipo pomwepo anamkhalira upo ndi Aherode, wakumuononga Iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Pamenepo Afarisi aja adatuluka nakachita upo ndi anthu a m'chipani cha Herode, kuti apangane njira yophera Yesu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Kenaka Afarisi anatuluka nayamba kukonza chiwembu ndi Aherode mmene angamuphere Yesu.

Onani mutuwo Koperani




Marko 3:6
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Afarisi anatuluka, nakhala upo womchitira Iye mwa kumuononga.


Ndipo anatumiza kwa Iye ophunzira ao, pamodzi ndi Aherode, amene ananena, Mphunzitsi, tidziwa kuti muli woona, ndipo muphunzitsa njira ya Mulungu moona ndithu, ndipo simusamala munthu aliyense; pakuti simuyang'anira pa nkhope ya anthu.


Ndipo anatuma kwa Iye ena a Afarisi ndi a Aherode, kuti akamkole Iye m'kulankhula kwake.


Ndipo Iye anawalamula, nanena, Yang'anirani, penyani kuti mupewe chotupitsa mkate cha Afarisi, ndi chotupitsa mkate cha Herode.


Ndipo ansembe aakulu ndi alembi anafunafuna maphedwe ake pakuti anaopa anthuwo.


Koma iwowo anagwidwa misala; nalankhulana wina ndi mnzake kuti amchitire Yesu chiyani.


Chifukwa chake, kuyambira tsiku lomwelo anapangana kuti amuphe Iye.


amene mwa Mzimu Woyera, pakamwa pa kholo lathu Davide mtumiki wanu, mudati, Amitundu anasokosera chifukwa chiyani? Nalingirira zopanda pake anthu?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa