Marko 3:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo anthu ambiri anakhala pansi pomzinga; nanena kwa Iye, Onani, amanu ndi abale anu ali kunja akufunani Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo anthu ambiri anakhala pansi pomzinga; nanena kwa Iye, Onani, amanu ndi abale anu ali kunja akufunani Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Anthu ambirimbiri adaakhala pansi pomzungulira. Ndiye iwo aja adamuuza kuti, “Amai anu ndi abale anu ali panjapa, akukufunani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Gulu la anthu linakhala momuzungulira Iye, ndipo anamuwuza kuti, “Amayi ndi abale anu ali panja akukufunani.” Onani mutuwo |