Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 3:19 - Buku Lopatulika

19 ndi Yudasi Iskariote, ndiye amene anampereka Iye. Ndipo analowa m'nyumba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 ndi Yudasi Iskariote, ndiye amene anampereka Iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 ndiponso Yudasi Iskariote (amene pambuyo pake adapereka Yesu kwa adani ake.)

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 ndi Yudasi Isikarioti, amene anamupereka Iye.

Onani mutuwo Koperani




Marko 3:19
13 Mawu Ofanana  

Simoni Mkanani, ndi Yudasi Iskariote amenenso anampereka Iye.


Ndipo Iye ali chilankhulire, onani, Yudasi, mmodzi wa khumi ndi awiriwo, anadza, ndi pamodzi ndi iye khamu lalikulu la anthu, ndi malupanga ndi mikunkhu, kuchokera kwa ansembe aakulu ndi akulu a anthu.


ndi Andrea, ndi Filipo, ndi Bartolomeo, ndi Mateyu, ndi Tomasi, ndi Yakobo mwana wa Alifeyo, ndi Tadeyo, ndi Simoni Mkanani,


Ndipo anthu ambiri anasonkhananso, kotero kuti sanathe iwo konse kudya.


Ndipo iwo anadza ku Kapernao; ndipo pamene anakhala m'nyumba, Iye anawafunsa, Munalikutsutsana ninji panjira?


Ndipo pokhala pamgonero, mdierekezi adatha kuika mu mtima wake wa Yudasi mwana wa Simoni Iskariote, kuti akampereke Iye,


Koma pali ena mwa inu amene sakhulupirira. Pakuti Yesu anadziwa poyamba amene ali osakhulupirira, ndi amene adzampereka.


Koma adanena za Yudasi, mwana wa Simoni Iskariote, pakuti iye ndiye amene akampereka Iye, ali mmodzi wa khumi ndi awiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa