Marko 2:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo anatulukanso kunka m'mbali mwa nyanja; ndipo linadza kwa Iye khamu lonse la anthu, ndipo anawaphunzitsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo anatulukanso kunka m'mbali mwa nyanja; ndipo linadza kwa Iye khamu lonse la anthu, ndipo anawaphunzitsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Yesu adapitanso ku nyanja. Anthu ambirimbiri adafika komweko, ndipo Iye adayamba kuŵaphunzitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Yesu anatulukanso napita kumbali ya nyanja. Gulu lalikulu la anthu linabwera kwa Iye, ndipo anayamba kuliphunzitsa. Onani mutuwo |