Marko 2:11 - Buku Lopatulika11 Ndikuuza iwe, Nyamuka, senza mphasa yako, numuke kwanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndikuuza iwe, Nyamuka, senza mphasa yako, numuke kwanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 “Iwe, dzuka, tenga machira ako, uzipita kumudzi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 “Ndikuwuza iwe, imirira, tenga mphasa yako ndipo pita kwanu.” Onani mutuwo |