Marko 16:10 - Buku Lopatulika10 Iyeyu anapita kuwauza iwo amene ankakhala naye, ali ndi chisoni ndi kulira misozi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Iyeyu anapita kuwauza iwo amene ankakhala naye, ali ndi chisoni ndi kulira misozi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mariayo adapita kukauza amene ankakhala ndi Yesu aja. Iwowo nkuti ali ndi chisoni ndipo akungolira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Iye anapita ndi kukawawuza amene anali ndi Yesu, amene ankakhuza maliro ndi kulira. Onani mutuwo |