Marko 15:44 - Buku Lopatulika44 Ndipo Pilato anazizwa ngati adamwaliradi; naitana kenturiyo, namfunsa ngati adamwalira kale. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Ndipo Pilato anazizwa ngati adamwaliradi; naitana kenturiyo, namfunsa ngati adamwalira kale. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Pilato adaadabwa kumva kuti Yesu wafa kale. Choncho adaitanitsa mkulu wa asilikali uja, namufunsa kuti, “Kodi Yesu wafa kaledi?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Pilato anadabwa pakumva kuti anali atamwalira kale. Anayitana Kenturiyo, namufunsa ngati Yesu anali atamwalira kale. Onani mutuwo |