Marko 14:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo ophunzira anatuluka, nafika m'mzinda, napeza monga anati kwa iwo; ndipo anakonza Paska. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo ophunzira anatuluka, nafika m'mzinda, napeza monga anati kwa iwo; ndipo anakonza Paska. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ophunzira aja adanyamuka naloŵa mumzindamo. Adachipezadi monga momwe Yesu adaaŵauzira, ndipo adakonza za phwando la Paska. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ophunzirawo anachoka, napita mu mzindawo ndipo anakapeza zinthu monga mmene Yesu anawawuzira. Choncho anakakonza Paska. Onani mutuwo |