Marko 14:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo pofika madzulo anadza Iye pamodzi ndi khumi ndi awiriwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo pofika madzulo anadza Iye pamodzi ndi khumi ndi awiriwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Kutada, Yesu adabwera ndi ophunzira ake khumi ndi aŵiri aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Ndipo kutada Yesu anafika ndi khumi ndi awiriwo. Onani mutuwo |