Marko 13:34 - Buku Lopatulika34 Monga ngati munthu wa paulendo, adachoka kunyumba kwake, nawapatsa akapolo ake ulamuliro, kwa munthu aliyense ntchito yake, nalamula wapakhomo adikire. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Monga ngati munthu wa paulendo, adachoka kunyumba kwake, nawapatsa akapolo ake ulamuliro, kwa munthu aliyense ntchito yake, nalamula wapakhomo adikire. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Ndi monga ngati bwana amene akunyamuka ulendo kuchoka kunyumba kwake. Amasiya zinthu m'manja mwa antchito ake, aliyense ntchito yake, ndipo amauza wapakhomo kuti azikhala maso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Zili ngati munthu amene akuchokapo. Amasiyira nyumba yake antchito ake, aliyense ndi ntchito yake; ndi kumuwuza wa pa khomo kuti azikhala maso. Onani mutuwo |