Marko 13:35 - Buku Lopatulika35 Chifukwa chake dikirani; pakuti simudziwa inu nthawi yake yakubwera mwini nyumba, kapena madzulo, kapena pakati pausiku, kapena pakulira tambala, kapena mamawa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Chifukwa chake dikirani; pakuti simudziwa inu nthawi yake yakubwera mwini nyumba, kapena madzulo, kapena pakati pausiku, kapena pakulira tambala, kapena mamawa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Nanunso tsono khalani maso, chifukwa simudziŵa mwini nyumba adzabwerera nthaŵi yanji: kaya ndi madzulo, kaya ndi pakati pa usiku, kaya ndi tambala woyamba, kapena mbandakucha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 “Inunso muyenera kukhala maso chifukwa simukudziwa nthawi imene mwini nyumba adzabwere, kaya madzulo, kapena pakati pa usiku, kapena tambala akulira, kapena mʼbandakucha. Onani mutuwo |