Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 11:19 - Buku Lopatulika

19 Ndipo masiku onse madzulo anatuluka Iye m'mzinda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Ndipo masiku onse madzulo anatuluka Iye m'mudzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Kutayamba kuda, Yesu ndi ophunzira ake adatulukamo mumzindamo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Pofika madzulo, iwo anatuluka mu mzindamo.

Onani mutuwo Koperani




Marko 11:19
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Iye anawasiya, natuluka m'mzinda, napita ku Betaniya, nagona kumeneko.


Ndipo Iye analowa mu Yerusalemu, mu Kachisi; ndipo m'mene anaunguza zinthu zonse, popeza ndi madzulo, anatuluka kupita ku Betaniya pamodzi ndi khumi ndi awiriwo.


Ndipo usana uliwonse Iye analikuphunzitsa mu Kachisi; ndi usiku uliwonse anatuluka, nagona paphiri lotchedwa la Azitona.


Pokhala muli nako kuunika, khulupirirani kuunikako, kuti mukakhale ana a kuunikako. Izi Yesu analankhula, nachoka nawabisalira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa