Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 10:44 - Buku Lopatulika

44 ndipo aliyense amene afuna kukhala woyamba mwa inu adzakhala kapolo wa onse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

44 ndipo amene aliyense afuna kukhala woyamba mwa inu adzakhala kapolo wa onse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

44 Ndipo aliyense wofuna kukhala mtsogoleri pakati panu, azikhala kapolo wa onse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

44 ndipo aliyense amene akufuna kukhala wamkulu akhale kapolo wa onse.

Onani mutuwo Koperani




Marko 10:44
5 Mawu Ofanana  

Ndipo kwa iye wofuna kupita nawe kumlandu ndi kutenga malaya ako, umlolezenso chofunda chako.


Koma mwa inu sikutero ai; koma aliyense amene afuna kukhala wamkulu mwa inu adzakhala mtumiki wanu;


Pakuti ndithu, Mwana wa Munthu sanadze kutumikiridwa, koma kutumikira, ndi kupereka moyo wake dipo la kwa anthu ambiri.


Ndipo m'mene anakhala pansi anaitana khumi ndi awiriwo; nanena nao, Ngati munthu afuna kukhala woyamba, akhale wakuthungo wa onse, ndi mtumiki wa onse.


koma anadzikhuthula yekha, natenga maonekedwe a kapolo, nakhala m'mafanizidwe a anthu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa