Marko 10:41 - Buku Lopatulika41 Ndipo pamene khumiwo anamva, anayamba kupsa mtima chifukwa cha Yakobo ndi Yohane. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ndipo pamene khumiwo anamva, anayamba kupsa mtima chifukwa cha Yakobo ndi Yohane. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Pamene khumi ena aja adamva zimenezi, adapsera mtima Yakobeyo ndi Yohaneyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Ophunzira khumiwo otsalawo atamva izi anapsera mtima Yakobo ndi Yohane. Onani mutuwo |