Marko 10:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo anadabwa, nanena kwa Iye, Ndipo angathe kupulumuka ndani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo anadabwa, nanena kwa Iye, Ndipo angathe kupulumuka ndani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Pamenepo ophunzira aja adazizwa koposa, nayamba kufunsana kuti, “Tsono nanga angathe kupulumuka ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Ophunzira anadabwa kwambiri, ndipo anati kwa wina ndi mnzake, “Nanga ndani amene angapulumuke?” Onani mutuwo |