Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 10:25 - Buku Lopatulika

25 Nkwa pafupi kuti ngamira ipyole diso la singano kuposa kuti mwini chuma alowe mu Ufumu wa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Nkwa pafupi kuti ngamira ipyole diso la singano kuposa kuti mwini chuma alowe mu Ufumu wa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Nkwapafupi kuti ngamira idzere pa kachiboo ka zingano, kupambana kuti munthu wachuma akaloŵe mu Ufumu wa Mulungu.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Ndi kwapafupi kwa ngamira kuti idzere pa kabowo ka zingano kusiyana ndi munthu wachuma kuti alowe mu ufumu wa Mulungu.”

Onani mutuwo Koperani




Marko 10:25
7 Mawu Ofanana  

Wokhulupirira chuma chake adzagwa; koma olungama adzaphuka ngati tsamba.


Kodi angathe Mkusi kusanduliza khungu lake, kapena nyalugwe mawanga ake? Pamenepo mungathe inunso kuchita zabwino, inu amene muzolowera kuchita zoipa.


Atsogoleri akhungu inu, akukuntha udzudzu, koma mumeza ngamira.


Ndipo anadabwa, nanena kwa Iye, Ndipo angathe kupulumuka ndani?


Pakuti nkwapafupi kwa ngamira ipyole diso la singano koma kwa munthu mwini chuma, kulowa Ufumu wa Mulungu nkwapatali.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa