Marko 10:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo anadza kwa Iye Afarisi, namfunsa Iye ngati kuloledwa kuti munthu achotse mkazi wake, namuyesa Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo anadza kwa Iye Afarisi, namfunsa Iye ngati kuloledwa kuti munthu achotse mkazi wake, namuyesa Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono kudafika Afarisi ena, namufunsa kuti, “Kodi nkololedwa kuti munthu asudzule mkazi wake?” Pomufunsa chonchi ankangofuna pomupezera chifukwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Afarisi ena anabwera kudzamuyesa pomufunsa kuti, “Kodi malamulo amalola kuti mwamuna asiye mkazi wake?” Onani mutuwo |