Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 1:3 - Buku Lopatulika

3 Mau a wofuula m'chipululu, konzani khwalala la Ambuye, lungamitsani njira zake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Mau a wofuula m'chipululu, konzani khwalala la Ambuye, lungamitsani njira zake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Liwu la munthu wofuula m'chipululu: akunena kuti, ‘Konzani mseu wodzadzeramo Ambuye, ongolani njira zoti adzapitemo.’ ”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 “Mawu a wofuwula mʼchipululu, ‘Konzani njira ya Ambuye, wongolani njira zake.’ ”

Onani mutuwo Koperani




Marko 1:3
8 Mawu Ofanana  

Ndipo masiku aja anadza Yohane Mbatizi, nalalikira m'chipululu cha Yudeya,


Pakuti uyu ndiye ananenayo Yesaya mneneri, kuti, Mau a wofuula m'chipululu, konzani khwalala la Ambuye, lungamitsani njira zake.


pa ukulu wansembe wao wa Anasi ndi Kayafa, panadza mau a Mulungu kwa Yohane mwana wa Zekariya m'chipululu.


Yohane achita umboni za Iye, nafuula nati, Uyu ndiye amene ndinanena za Iye, Wakudzayo pambuyo panga analipo ndisanabadwe ine; chifukwa anakhala woyamba wa ine.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa