Marko 1:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo Yesu anaudzudzula, kuti, Khala uli chete, nutuluke mwa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo Yesu anaudzudzula, kuti, Khala uli chete, nutuluke mwa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Koma Yesu adazazira mzimu woipawo, adati, “Khala chete, tuluka mwa munthuyu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Yesu anadzudzula chiwandacho mwamphamvu nati, “Khala chete! Tuluka mwa iye!” Onani mutuwo |