Marko 1:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo Yesu ananena nao, Idzani pambuyo panga, ndipo ndidzakusandutsani inu asodzi a anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo Yesu ananena nao, Idzani pambuyo panga, ndipo ndidzakusandutsani inu asodzi a anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Yesu adaŵauza kuti, “Inu, munditsate, ndikakusandutseni asodzi a anthu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Yesu anati, “Bwerani, tsateni Ine, ndipo ndidzakusandutsani asodzi a anthu.” Onani mutuwo |