Marko 1:15 - Buku Lopatulika15 nanena, Nthawi yakwanira, ndipo Ufumu wa Mulungu wayandikira; tembenukani mtima, khulupirirani Uthenga Wabwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 nanena, Nthawi yakwanira, ndipo Ufumu wa Mulungu wayandikira; tembenukani mtima, khulupirirani Uthenga Wabwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Ankati, “Nthaŵi yakwana, Ufumu wa Mulungu wayandikira. Tembenukani mtima ndi kukhulupirira Uthenga Wabwinowu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 “Nthawi yafika, ufumu wa Mulungu wayandikira. Tembenukani mtima ndi kukhulupirira Uthenga Wabwino!” Onani mutuwo |