Marko 1:1 - Buku Lopatulika1 Chiyambi chake cha Uthenga Wabwino wa Yesu Khristu, Mwana wa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Chiyambi chake cha Uthenga Wabwino wa Yesu Khristu, Mwana wa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Uwu ndi Uthenga Wabwino wonena za Yesu Khristu, Mwana wa Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Chiyambi cha Uthenga Wabwino wa Yesu Khristu, Mwana wa Mulungu, Onani mutuwo |