Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Maliro 3:4 - Buku Lopatulika

4 Wagugitsa thupi langa ndi khungu langa, nathyola mafupa anga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Wagugitsa thupi langa ndi khungu langa, nathyola mafupa anga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Adandipweteka m'thupi lonse, ndipo adaphwanya mafupa anga onse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Wakalambitsa khungu langa ndi mnofu wanga, ndipo waphwanya mafupa anga.

Onani mutuwo Koperani




Maliro 3:4
10 Mawu Ofanana  

Khungu langa lada, nilindifundukira; ndi mafupa anga awawa ndi kutentha kwao.


Ndathiridwa pansi monga madzi, ndipo mafupa anga onse anaguluka. Mtima wanga ukunga sera; wasungunuka m'kati mwa matumbo anga.


Pamene ndinakhala chete mafupa anga anakalamba ndi kubuula kwanga tsiku lonse.


Mundimvetse chimwemwe ndi kusekera, kuti mafupawo munawathyola akondwere.


Ndinadzitonthoza kufikira mamawa; monga mkango, momwemo Iye anathyolathyola mafupa anga onse; Kuyambira usana kufikira usiku mudzanditsiriza ine.


Israele ndiye nkhosa yolowerera, mikango yampirikitsa, poyamba inamudya mfumu ya Asiriya; ndipo pomaliza Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni wathyola mafupa ake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa