Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 9:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo anakhala masiku atatu wosaona, ndipo sanadye kapena kumwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo anakhala masiku atatu wosaona, ndipo sanadya kapena kumwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Ndipo adakhala masiku atatu osatha kupenya ndiponso osadya kapena kumwa kanthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Anakhala wosaona kwa masiku atatu ndiponso sanadye kapena kumwa kanthu kalikonse.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 9:9
7 Mawu Ofanana  

Muka, sonkhanitsa Ayuda onse opezeka mu Susa, nimundisalire, osadya osamwa masiku atatu, usiku ndi usana, ine ndemwe ndi anamwali anga tidzasala momwemo, ndipo motero ndidzalowa kwa mfumu, ndiko kosalingana ndi lamulo; ndikaonongeka tsono ndionongeke.


Koma ku Damasiko kunali wophunzira wina dzina lake Ananiya; ndipo Ambuye anati kwa iye m'masomphenya, Ananiya. Ndipo anati, Ndili pano, Ambuye,


Ndipo Saulo anauka; koma potseguka maso ake, sanapenye kanthu; ndipo anamgwira dzanja, namtenga nalowa naye mu Damasiko.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa