Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 8:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo panakhala chimwemwe chachikulu m'mzindamo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo panakhala chimwemwe chachikulu m'mudzimo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Choncho munali chimwemwe chachikulu mumzinda muja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Kotero munali chimwemwe chachikulu mu mzindawo.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 8:8
10 Mawu Ofanana  

Chifukwa chake pamene Asamariya anadza kwa Iye, anamfunsa akhale nao; ndipo anakhala komweko masiku awiri.


Ndipo pakumva ichi amitundu anakondwera, nalemekeza mau a Mulungu; ndipo anakhulupirira onse amene anaikidwiratu kumoyo wosatha.


Ndipo ophunzira anadzazidwa ndi chimwemwe ndi Mzimu Woyera.


Ndipo pamene anakwera kutuluka m'madzi, Mzimu wa Ambuye anakwatula Filipo; ndipo mdindo sanamuonenso, pakuti anapita njira yake wokondwera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa