Machitidwe a Atumwi 7:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo mtundu umene udzawayesa akapolo, ndidzauweruza Ine, anatero Mulungu; ndipo zitapita izi adzatuluka, nadzanditumikira Ine m'malo muno. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo mtundu amene udzawayesa akapolo, ndidzauweruza Ine, anatero Mulungu; ndipo zitapita izi adzatuluka, nadzanditumikira Ine m'malo muno. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mulungu adatinso, ‘Koma Ine ndidzaulanga mtundu wa anthuwo umene udzazisandutsa akapolo. Bwino lake zidzatuluka m'dzikomo nkudzandipembedza pamalo pano.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mulungu anati, ‘Ine ndidzalanga dziko limene zidzukulu zako zidzagwireko ukapolo, ndipo pambuyo pake akadzatuluka mʼdzikolo adzandipembedza Ine pamalo pano.’ Onani mutuwo |